Tsimikizani
Pangani Dawunilodi:
1. Mumapemphera.
M’malalikira.
Mwakhulupirika muzonse.
Mayesero anu ndi ambiridi,
Koma Yehova akuona.
(KUKONZEKERA KOLASI)
Mukamaweruzidwa kumakhoti,
Simuli nokha.
Ndinutu zitsanzo zabwino,
N’zolimbikitsa.
(KOLASI)
‘Ndatsimikiza
Imfa, moyo, maboma satilekanitsa ndi M’lungu.’
‘Ndatsimikiza
Zam’tsogolo, kaya mphamvu, sizitilekanitsa.’
Tsimikizani
Kukondabe M’lungu.
2. Mwachita bwino.
Simunagonje.
M’madalira M’lungu
Nthawi zonse.
Adani ayesa kutiletsatu,
Dziwani tili mbali yanu.
(KUKONZEKERA KOLASI)
Mukamaweruzidwa kumakhoti,
Simuli nokha.
Ndinutu zitsanzo zabwino,
N’zolimbikitsa.
(KOLASI)
‘Ndatsimikiza
Imfa, moyo, maboma satilekanitsa ndi M’lungu.’
‘Ndatsimikiza
Zam’tsogolo, kaya mphamvu, sizitilekanitsa.’
Tsimikizani
Kukondabe M’lungu.
Mudziwetu.
(VESI LOKOMETSERA)
Tikhoza kuzunzidwa pomvera Mulungu—
Pokonda M’lungu.
‘Komabetu mukugonjetsa zinthu zonsezi’—