Yang’ane
Pangani Dawunilodi:
1. Ga—nizako zina.
Chonde lankhula.
Usasemphane n’zinthu zabwino
Palitu zabwino zina
M’malo mofatsa
Kucheza ndi anthu pafoni. Oh ya!
Usawononge nthawi ndi zinthu zopanda ntchito.
Cheza ndi anzako enieni.
(KOLASI)
Yang’ane.
Ticheze
Uwone
Banja limodzi, padziko lonse.
Yang’ane
Udziwe
Tadziwa
Anzakofe. isiye foni, yang’ane.
2. Wo—natu zimene,
Ena ‘kuwona.
Usasokonezeke ndi foni.
Anzako enienidi,
Okonda Yehova,
Angakuthandize mpaka kale.
Sunga—dziwane nawo ukafatsa n’zinthu zopanda ntchito.
Cheza ndi anzako enieni.
(KOLASI)
Yang’ane.
Ticheze
Uwone
Banja limodzi, padziko lonse.
Yang’ane
Udziwe
Tadziwa
Anzakofe.
(MAWU OWONJEZERA)
Isiye foni, yang’ane.
(VESI LOKOMETSERA)
(Usalorere) kuti akupusitsedi
Pena nkhani zaketu ndi zongopeza.
(Anthu ake nawonso) anthu ake ndi ankhanza.
Bwanji osaganiza zosintha maganizowo?
3. I—siye foniyo
Ngatitu susintha,
Ungasemphane m’moyo wabwino.
Za—bwino n’zambiri—
Zomwe timakonda
Zakhala zilipo. Usaiwaletu.
Foni wanyamulayo isakusokoneze.
Uli ndi anzako enieni
(KOLASI)
Yang’ane.
Ticheze
Uwone
Banja limodzi, padziko lonse.
Yang’ane
Udziwe
Tadziwa
Anzakofe. isiye foni, yang’ane.
Ticheze
Uwone
Banja limodzi, padziko lonse.
Yang’ane
Udziwe
Tadziwa
Anzakofe. isiye foni, yang’ane.