Yehova Wakulandira
Pangani Dawunilodi:
1. Sikale pomwe unamva,
N’kukonda dzina langa,
Komatu unasiya cho’nadi.
Zomwe umakumbukira
Zimakusangalatsa,
Zikuthandizetu kubwerera.
(KOLASI)
Ndakulandira.
Ungayambirenso.
Ndikuteteza
Udzasangalala mpaka muyaya.
2. Ndikufunatu udziwe
Zofunika kuchita
Zokuthandiza kubwereranso.
Ndikudikira mwachidwi;
Ndidzakutetezenso
Udzamva bwino
Ukayambanso.
(KOLASI)
Ndakulandira.
Ungayambirenso.
Ndikuteteza
Udzasangalala
Mpaka muyaya.
Wafika.