Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Yehova Watithandiza Kukhala Amodzi

Yehova Watithandiza Kukhala Amodzi

Pangani Dawunilodi:

  1. 1. Padzikoli pali kusamvana.

    Anthu ambiri sagwirizana.

    Iwo akufuna zisinthetu.

    Koma ife timadalira M’lungu.

    (KUKONZEKERA KOLASI)

    Tizimvera Mawu ake

    Tikane mbali ya dziko.

    (KOLASI)

    Tizikondana pachilichonse,

    Polalikira uthenga.

    Timakonda abale athu.

    Yehova watithandiza

    Kukhala amodzi.

  2. 2. Kulikonse komwe tingapite,

    Timakapeza abale athu.

    Nkhawa zathu zonse zidzathadi.

    M’dziko latsopano posachedwa.

    (KUKONZEKERA KOLASI)

    Tizimvera Mawu ake

    Tikane mbali ya dziko.

    (KOLASI)

    Tizikondana pachilichonse,

    Polalikira uthenga.

    Timakonda abale athu.

    Yehova watithandiza

    Kukhala amodzi.

    Amodzi.

    (KUKONZEKERA KOLASI)

    Tikhulupirike ndithu

    Tikane mbali ya dziko.

    (KOLASI)

    Tizikondana pachilichonse,

    Polalikira uthenga.

    Timakonda abale athu.

    Yehova watithandiza

    Ndiyetu

    (KOLASI)

    Tizikondana pachilichonse,

    Polalikira uthenga.

    Timakonda abale athu.

    Yehova watithandiza

    Kukhala amodzi.

    Amodzi.