Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

TIMABUKU TOTHANDIZA ANTHU KUTIDZIWA BWINO PADZIKO LONSE

Mmene a Mboni za Yehova Amaonera Nkhani ya Banja

Mmene a Mboni za Yehova Amaonera Nkhani ya Banja

A Mboni za Yehova amayesetsa kutsatira mfundo za m’Baibulo zomwe zimathandiza kuti mabanja awo azikhala osangalala. Makolo a Mboni amaona kuti ali ndi udindo waukulu wophunzitsa ana awo mfundo za m’Baibulo.