Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

TIMABUKU TOTHANDIZA ANTHU KUTIDZIWA BWINO PADZIKO LONSE

A Mboni za Yehova Komanso Mabuku ndi Zinthu Zina Zomwe Amapanga

A Mboni za Yehova Komanso Mabuku ndi Zinthu Zina Zomwe Amapanga

Mabuku ndi zinthu zina zimene a Mboni za Yehova amapanga zimapezeka pa intaneti komanso zosindikiza. Zinthu zimenezi zimathandiza anthu kuyandikira Mulungu komanso kulimvetsa bwino Baibulo. Zimathandizanso kuti anthu asinthe miyoyo yawo n’kumakhala moyo wabwino.