Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

TIMABUKU TOTHANDIZA ANTHU KUTIDZIWA BWINO PADZIKO LONSE

A Mboni za Yehova Komanso Malo Awo Olambirira

A Mboni za Yehova Komanso Malo Awo Olambirira

A Mboni za Yehova amaona kuti kusonkhana ndi anzawo n’kofunika kwambiri pa kulambira kwawo. Cholinga cha misonkhano yawo, yomwe imachitikira m’maholo omwe amatchedwa Nyumba za Ufumu, chimakhala kuphunzira Mawu a Mulungu ndipo aliyense ndi wolandiridwa.