Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

TIMABUKU TOTHANDIZA ANTHU KUTIDZIWA BWINO PADZIKO LONSE

A Mboni za Yehova Komanso Mmene Amathandizira Anthu M’madera Omwe Amakhala

A Mboni za Yehova Komanso Mmene Amathandizira Anthu M’madera Omwe Amakhala

A Mboni za Yehova amayesetsa kuthandiza anthu m’madera omwe amakhala pogwira ntchito yophunzitsa anthu Baibulo komanso kuthandiza anthu pakagwa ngozi.