Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

TIMABUKU TOTHANDIZA ANTHU KUTIDZIWA BWINO PADZIKO LONSE

A Mboni za Yehova Komanso Ntchito Yawo Yothandiza Anthu Pakagwa Ngozi Zadzidzidzi

A Mboni za Yehova Komanso Ntchito Yawo Yothandiza Anthu Pakagwa Ngozi Zadzidzidzi

Ngozi ikachitika, a Mboni za Yehova amachita zinthu mwachangu kuti athandize anthu okhudzidwa powapatsa zimene akufunikira komanso kuwalimbikitsa ndi mfundo za m’Baibulo. Maboma komanso mabungwe othandiza anthu pakagwa ngozi amaona kuti a Mboni amachita zinthu mwadongosolo kwambiri pochita zimenezi.