Kuona Malo ku Beteli
Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi omwenso amadziwika kuti Beteli. Ku maofesi athu ena kulinso malo achionetsero omwe mukhoza kuona nokha popanda wokutsogolerani.
Kuyambiranso Kuona Malo: M'mayiko ambiri, anthu adzayambiranso kuona malo m'maofesi athu a nthambi kuyambira pa 1 June, 2023. Kuti mudziwe zambiri, lankhulani ndi abale a ku nthambi yomwe mukufuna kukaonayo. Komabe, musapite kukaona malo ngati mwapezeka ndi COVID-19 kapena ngati muli ndi zizindikiro za chimfine kapenanso ngati posachedwapa munakumana ndi munthu amene wapezeka ndi COVID-19.
Benin
ARTJB (Association religieuse des Témoins de Jéhovah du Bénin)
Route Inter-Etat Cotonou-Parakou
AB-CALAVI
BENIN
+229 97-97-95-33
+229 97-97-95-34
+229 21-36-04-57 (Fax)
Kuona Malo
Lolemba mpaka Lachisanu
8:00 a.m. mpaka 10:45 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 3:45 p.m.
Nthawi yonse: Mphindi 45
Zimene Timachita
Timamasulira mabuku a nkhani za m’Baibulo m’Chibariba, Chifoni, Chigani, Chijula, Chikabiye, Chimore ndi Chizama. Timatumiza mabuku kumagulu ndi ku mipingo yoposa 500, ku Benin, Burkina Faso, Niger, ndi Togo.