Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Kuona Malo ku Beteli

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi omwenso amadziwika kuti Beteli. Ku maofesi athu ena kulinso malo achionetsero omwe mukhoza kuona nokha popanda wokutsogolerani.

Kuyambiranso Kuona Malo: M'mayiko ambiri, anthu adzayambiranso kuona malo m'maofesi athu a nthambi kuyambira pa 1 June, 2023. Kuti mudziwe zambiri, lankhulani ndi abale a ku nthambi yomwe mukufuna kukaonayo. Komabe, musapite kukaona malo ngati mwapezeka ndi COVID-19 kapena ngati muli ndi zizindikiro za chimfine kapenanso ngati posachedwapa munakumana ndi munthu amene wapezeka ndi COVID-19.

Cuba

Ave. 15 #4608 e/ 46 y 48

PLAYA, LA HABANA

CUBA

+53 7 204 7598

+53 7 204 1026

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

9:00 a.m. mpaka 11:⁠00 a.m. komanso 2:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yoona malo: Ola limodzi

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku ofotokoza Baibulo m’chinenero chamanja cha ku Cuba. Timayang’anira ntchito imene a Mboni za Yehova okwana ??? amagwira m’dziko la Cuba.