Pitani ku nkhani yake

Kuona Malo ku Beteli

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi omwenso amadziwika kuti Beteli. Ku maofesi athu ena kulinso malo achionetsero omwe mukhoza kuona nokha popanda wokutsogolerani.

Kuyambiranso Kuona Malo: M'mayiko ambiri, anthu adzayambiranso kuona malo m'maofesi athu a nthambi kuyambira pa 1 June, 2023. Kuti mudziwe zambiri, lankhulani ndi abale a ku nthambi yomwe mukufuna kukaonayo. Komabe, musapite kukaona malo ngati mwapezeka ndi COVID-19 kapena ngati muli ndi zizindikiro za chimfine kapenanso ngati posachedwapa munakumana ndi munthu amene wapezeka ndi COVID-19.

The Democratic Republic of the Congo

75, 13e Rue, Q. Industriel

LIMETE

KINSHASA

DEMOCRATIC REPUBLIC OF THE CONGO

+243 +243 81-555-1000

+243 99-818-9791

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

9:00 a.m. mpaka 10:30 a.m. ndi 1:30 p.m. mpaka 3:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi

Zimene Timachita

Timamasulira magazini a Nsanja ya Olonda m’zinenero 8, komanso mabuku ena m’zinenero zina 30. Timatumiza mabuku olemera matani 1,800 chaka chilichonse m’mipingo yoposa ??? m’dziko lonse la Congo Kinshasa.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.