Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Kuona Malo ku Beteli

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi omwenso amadziwika kuti Beteli. Ku maofesi athu ena kulinso malo achionetsero omwe mukhoza kuona nokha popanda wokutsogolerani.

Kuyambiranso Kuona Malo: M'mayiko ambiri, anthu adzayambiranso kuona malo m'maofesi athu a nthambi kuyambira pa 1 June, 2023. Kuti mudziwe zambiri, lankhulani ndi abale a ku nthambi yomwe mukufuna kukaonayo. Komabe, musapite kukaona malo ngati mwapezeka ndi COVID-19 kapena ngati muli ndi zizindikiro za chimfine kapenanso ngati posachedwapa munakumana ndi munthu amene wapezeka ndi COVID-19.

South Africa

1 Robert Broom Drive East

Rangeview

KRUGERSDORP

1739

SOUTH AFRICA

+27 11-761-1000

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

7:45 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Maola awiri

Zimene Timachita

Timasindikiza mabuku, magazini ndiponso timapepala m’zinenero 121 ndipo timatumiza zinthu zimenezi kumipingo yoposa 12,000 m’mayiko 11. Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’zinenero 20. Timathandizanso ntchito yomanga Nyumba za Ufumu m’mayiko 42.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.