Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Lipoti la Pamsonkhano Wamayiko

Lipoti la Pamsonkhano Wamayiko

Pamsonkhano wathu wamayiko womwe umachitika kwa masiku angapo, anthu ochokera m’mayiko osiyanasiyana, m’mitundu yosiyanasiyana ndiponso a zinenero zosiyanasiyana amakhala pamodzi n’kumasangalala ndi kuphunzira Baibulo komanso kucheza.