Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Tikukuitanani ku Msonkhano wa Mboni za Yehova wa 2023 Wakuti, “Khalani Oleza Mtima”

Tikukuitanani ku Msonkhano wa Mboni za Yehova wa 2023 Wakuti, “Khalani Oleza Mtima”

Panopa tikufunikira kukhala oleza mtima kwambiri kuposa kale. Koma kodi kuleza mtima kumatanthauza chiyani? Nanga kumakhudza bwanji moyo wathu wa tsiku ndi tsiku? Bwerani ku Msonkhano wa 2023 Wakuti, “Khalani Oleza Mtima.”