Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? YAMBANI Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? Onerani vidiyo yosonyeza mmene phunziro la Baibulo limachitikira. Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi MAFUNSO OFUNSIDWA KAWIRIKAWIRI Kodi Phunziro la Baibulo lomwe a Mboni za Yehova Amachititsa Limakhala Lotani? Mukamaphunzira Baibulo kwaulere ndi a Mboni za Yehova, mungagwiritse ntchito Baibulo lililonse limene mukufuna. Mungapemphenso onse a m’banja lanu kapena mnzanu wina aliyense kuti akhale nanu pa phunzirolo. ZOKHUDZA IFEYO Pemphani Kuti Tidzakuyendereni Mutha kukhala ndi mwayi wokambirana nkhani inayake ya m’Baibulo kapena kudziwa zambiri zokhudza Mboni za Yehova. MISONKHANO Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani? Onani mkati mwa Nyumba ya Ufumu kuti mudziwe zimene zimachitika. ZOKHUDZA IFEYO N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo—Vidiyo Yathunthu Baibulo likuthandiza anthu ambirimbiri padziko lonse lapansi kupeza mayankho a mafunso ofunika kwambiri. Kodi inunso mungakonde? Sindikizani Patsani ena Patsani ena Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? ZOKHUDZA IFEYO Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? Chichewa Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/502014311/univ/art/502014311_univ_sqr_xl.jpg