Mboni za Yehova Padziko Lonse

Botswana

  • Sepupa, Botswana​—Kulalikira msodzi mumtsinje wa Okavango

Mfundo Zachidule—Botswana

  • 2,346,000—Chiwerengero cha anthu
  • 2,391—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 42—Mipingo
  • Pa anthu 1,016 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NTCHITO YOLALIKIRA

Pachionetsero cha ku Botswana Panali Chuma Chamtengo Wapatali

Ana omwe anafika pamalowa anachita chidwi kwambiri ndi mavidiyo a makatuni a mutu wakuti Khalani Bwenzi la Yehova omwe amathandiza anthu kugwiritsa ntchito mfundo za m’Baibulo.