Mboni za Yehova Padziko Lonse

Costa Rica

  • Zarcero, Costa Rica​—Kukambirana mfundo za m’Baibulo ndi woweta ng’ombe m’dera la kunja kwa mzinda

Mfundo Zachidule—Costa Rica

  • 5,213,000—Chiwerengero cha anthu
  • 32,084—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 429—Mipingo
  • Pa anthu 163 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

GALAMUKANI!

Dziko la Costa Rica

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe chifukwa chake anthu a m’dzikoli amadziwika kuti Atiko.