Mfundo Zachidule—Malta
- 542,000—Chiwerengero cha anthu
- 877—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 11—Mipingo
- Pa anthu 643 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
Birgu, Malta—Akugawira kapepala kakuti, Kodi Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambiri Okhudza Moyo?