Mboni za Yehova Padziko Lonse

Namibia

  • M’chigawo cha Kunene, ku Namibia​—Akulalikira anthu a mtundu wa Chihimba pogwiritsa ntchito kabuku kakuti Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha, m’chinenero cha Chiherero

Mfundo Zachidule—Namibia

  • 2,680,000—Chiwerengero cha anthu
  • 2,711—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 47—Mipingo
  • Pa anthu 1,030 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi