Mfundo Zachidule—United States of America
- 336,679,000—Chiwerengero cha anthu
- 1,233,609—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 11,942—Mipingo
- Pa anthu 276 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
ZOCHITIKA PA MOYO
Mfundo Zothandiza Anthu Ogwira Ntchito Zachipatala Omwe Ali Ndi Nkhawa
Kodi manesi Komanso ogwira ntchito pachipatala china anapeza bwanji mfundo zolimbikitsa pa nthawi ya mliri wa COVID-?
MOYO WA PA BETELI
Tikukuitanani Kuti Mudzaone Maofesi Athu ku United States
Mudzaonanso Likulu la Padziko Lonse la Mboni za Yehova lomwe lili ku United States.
NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)
Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku New York
N’chiyani chinachititsa anthu okhala m’nyumba yabwino kwambiri kuti alolere kusamukira m’kanyumba kakang’ono kwambiri