Chikhulupiriro Chinathandiza Kwambiri Anthu Omwe Anakhudzidwa ndi Mvula Yamkuntho ku Philippines
Onani zimene anthu omwe anapulumuka ananena.
Nkhani Zina
Kupirira Mavuto Aakulu Mtendere Komanso Moyo Wosangalala Kuthandiza Ena Zimene a Mboni za Yehova AmachitaMwina Mungakondenso Kudziwa Izi
KUTHANDIZA ENA
Pa Nthawi ya Tsoka, Timathandizana Chifukwa cha Chikondi
M’mayiko ambirimbiri, a Mboni za Yehova amathandiza anthu amene ali m’mavuto.
NKHANI
Anthu Amene Anakhudziwa ndi Mphepo Yamkuntho Yotchedwa Typhoon Haiyan Tsopano Amangiridwa Nyumba
Mphepo yamkuntho yotchedwa Typhoon Haiyan itawononga zinthu, a Mboni za Yehova anagwira ntchito yaikulu yomanga nyumba pafupifupi 750.
NKHANI
Nkhani Mwachidule: A Mboni za Yehova Akonza Ntchito Yothandiza Anthu Amene Anakhudzidwa ndi Mvula Yamkuntho ya Haiyan
Ntchito yothandiza anthu amene anakhudzidwa ndi ngozi ikuchitika ku Philippines ndipo amene akugwira ntchitoyi ndi anthu ongodzipereka. Katundu wokwana matani 190 wothandizira anthu wakhala akutumizidwa ku Phillipines.
NKHANI
Mvula Yoopsa Yamkuntho, Yotchedwa Haiyan Yasakaza Zinthu Kwambiri M’dera Lapakati ku Philippines
Mvula yoopsa yamkuntho, yotchedwa Haiyan inapha anthu komanso kuwononga zinthu ku Philippine. A Mboni za Yehova akugwira ntchito yothandiza anthu okhudzidwa ndi tsokali mogwirizana ndi akuluakulu a boma.
KUTHANDIZA ENA
Madzi Osefukira ku Alberta
Kodi a Mboni za Yehova anathandiza bwanji anthu amene anakhudzidwa ndi madzi osefukira m’dera la Alberta ku Canada?