Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

MAY 31, 2018
CANADA

Khoti Lalikulu Kwambiri ku Canada Lagamula Mlandu Mokomera Mboni za Yehova

Khoti Lalikulu Kwambiri ku Canada Lagamula Mlandu Mokomera Mboni za Yehova

Pa 31 May, 2018, Khoti Lalikulu Kwambiri ku Canada linapanga chigamulo chimene aliyense anagwirizana nacho choti makhoti asamalowerere dongosolo limene a Mboni za Yehova amatsatira lochotsa mu mpingo munthu yemwe wachita tchimo koma sanalape. Tikusangalala kwambiri kuti chigamulochi chithandiza kuti tipitirize kutsatira mfundo zolungama za Yehova.—Yesaya 33:22.

https://scc-csc.lexum.com/scc-csc/scc-csc/en/item/17101/index.do

Onani Zambiri