DECEMBER 25, 2020
NKHANI ZA PADZIKO LONSE
Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 9 la 2020
Pamene mliri wa COVID-19 ukupitirira, M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akufotokoza chifukwa chake tiyenera kupitirizabe kukhala osamala komanso zimene tingachite kuti tidziteteze ku mliriwu. Zitsanzo ziwiri zikutithandiza kuona ubwino wochita zimenezi.