Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Russia

 

2014-05-29

RUSSIA

Anthu Ena ku Russia Akuphwanyiridwa Ufulu Wawo Wolambira

A Mboni za Yehova akuimbidwa milandu m’tauni yaing’ono ya Taganrog. Akuluakulu a boma alanda mabuku ndiponso Nyumba ya Ufumu ya a Mboni za Yehova.

2014-05-29

RUSSIA

Anthu Ena a ku Russia Akuimbidwa Mlandu Chifukwa cha Chikhulupiriro Chawo

Ngati anthu a Mboni za Yehova omwe akuimbidwa milandu m’dera la Taganrog angapezeke kuti ndi olakwa, ndiye kuti zimenezi zidzasokoneza ufulu wachibadwidwe wa anthu ambiri m’dziko la Russia.

2014-04-10

RUSSIA

Khoti Lalikulu ku Russia Lakana Zoti Webusaiti ya JW.ORG Itsekedwe

Khoti lalikulu la Tver ku Russia lakana zimene khoti laling’ono linagamula zoti webusaiti yovomerezeka ya Mboni za Yehova, ya jw.org, itsekedwe.

2014-04-08

RUSSIA

Kupitiriza Nkhani: Mapulani Ofuna Kuletsa Webusaiti ya JW.ORG Alephereka

Khoti lalikulu linasintha chigamulo choti webusaiti ya jw.org iletsedwe m’dziko la Russia.

2014-04-08

RUSSIA

Akuluakulu a Boma la Russia Akufuna Kuletsa Webusaiti ya JW.ORG

Khoti la Tsentralniy District lomwe lili mumzinda wa Tver linagamula kuti webusaiti ya jw.org iletsedwe m’dziko la Russia. Koma a Mboni za Yehova achita apilo.

2013-08-29

RUSSIA

Khoti la ku Ulaya Lateteza Ufulu wa Mboni za Yehova pa Mlandu Wokhudza Kusungiridwa Chinsinsi

Khoti Loona za Ufulu wa Anthu ku Ulaya lalamula boma la Russia kuti lipereke chipukuta misozi kwa anthu amene linawaphwanyira ufulu wachibadwidwe wofunika kwambiri wokhudza kusungiridwa chinsinsi.

2013-12-31

RUSSIA

Khoti Linagamula kuti, “Sitili M’chaka cha 1937”

Woweruza milandu wa m’bwalo la milandu lalikulu ku Russia anatsutsa chigamulo chimene khoti laling’ono linalamula

2017-12-28

RUSSIA

Mavuto Amene a Mboni Akhala Akukumana Nawo kwa Zaka 10 pa Nkhani Zamalamulo Anaunikidwa pa Tsiku la 5 Lozenga Mlandu ku Khoti Lalikulu Kwambiri ku Russia

Maloya oimira Unduna wa Zachilungamo sanathe kunena chifukwa chomveka chokhudza malamulo chochititsa kuti Likulu la Mboni za Yehova litsekedwe ku Russia.

2017-02-07

RUSSIA

Akatswiri Ena Akana Kuti Boma la Russia Liletse Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Nkhaniyi ndi yachiwiri pa nkhani zitatu zomwe zikufotokoza zimene ananena akatswiri a zachipembedzo, a zandale, zachikhalidwe cha anthu komanso a maphunziro a ulamuliro wa Soviet Union.

2017-07-24

RUSSIA

Khoti Lalikulu Kwambiri M’dziko la Russia Silinasinthe Chigamulo Chimene Linapereka Choletsa Ntchito ya Mboni za Yehova

Khoti Lalikulu Kwambiri M’dziko la Russia silinasinthe chigamulo chimene linapereka pa 20 April, 2017. A Mboni za Yehova ku Russia apanga apilo za nkhaniyi ku Khoti Loona za Ufulu wa Anthu ku Ulaya komanso ku Komiti ya United Nations Yoona za Ufulu wa Anthu.

2017-09-21

RUSSIA

A Mboni za Yehova Akuvutika Kwambiri Chifukwa cha Chigamulo cha Khoti Lalikulu Kwambiri ku Russia

Chigamulo cha khoti chachititsa kuti anthu ambiri azidana ndi a Mboni ndipo chapereka mphamvu kwa anthu komanso akuluakulu a boma kuti aziwachitira nkhanza.