Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Russia

 

2022-03-24

RUSSIA

Abale Anathandiza M’bale Konstantin Bazhenov Ali M’ndende, Atatulutsidwa Komanso Pomwe Ankatumizidwa Kwawo

M’bale Konstantin Bazhenov ndi mmodzi mwa a Mboni za Yehova omwe anamalizitsa zaka zake zokhala m’ndende kuchokera pamene Khoti Lalikulu Kwambiri linaletsa ntchito yathu mu 2017. Atakhala m’ndende kwa chaka ndi miyezi 6, anatulutsidwa mofulumirirako pa 5 May 2021. Pambuyo pake anatumizidwa kwawo.

2022-04-22

RUSSIA

A Mboni za Yehova a ku Irkutsk Anakhalabe Okhulupirika Ngakhale Apolisi Anawachitira Nkhanza

Pa 4 October 2021, apolisi anakafufuza zinthu m’nyumba zingapo m’chigawo cha Irkutsk. Anapanikiza anthu ndi mafunso komanso kuwamenya mwankhanza kwambiri. Pamapeto pake a Mboni za Yehova okwana 6, anakawatsekera m’ndende chifukwa chotsatira zomwe amakhulupirira.

2021-09-06

Mlongo Valentina Baranovskaya Komanso Mwana Wawo Roman, Anamangidwa Popanda Zifukwa Zomveka

Onani mmene akuluakulu a boma la Russia a kuzunzira mlongo wachikulire wazaka 70 komanso mwana wawo chifukwa chochita zinthu zokhudzana ndi chikhulupiriro chawo mwamtendere.