JULY 26, 2021
RUSSIA
“Kuzunzidwaku Kwandithandiza Kuti Ndikhale pa Ubwenzi Wolimba Kwambiri ndi Yehova”
Nthawi Komanso Zimene Zinachitika
Khoti la M’boma la Pavlovskiy M’chigawo cha Krasnodar, posachedwapa lilengeza zokhudza mlandu wa M’bale Vladimir Skachidub. Loya woimira boma pa mlanduwu sananenebe chilango chimene akufuna kuti m’baleyu apatsidwe
30 December, 2020
Kumvetsera mlandu koyamba
23 July, 2020
Anaikidwa pa mndandanda wa anthu ochita zinthu zoopsa m’dziko la Russia
23 June, 2020
Anauzidwa kuti amupeza ndi mlandu chifukwa ankagwira ntchito yolalikira
Zokhudza M’baleyu
Mofanana ndi M’bale Vladimir, nafenso tikukhulupirira ndi mtima wonse kuti Yehova apitiriza kumuthandiza ‘kuti athe kupirira zinthu zonse ndi kukhala oleza mtima ndiponso wachimwemwe.’—Akolose 1:11.