Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

JANUARY 7, 2020
RUSSIA

Zimene Zinachitika Pamene M’bale Kuzin ndi M’bale Makhnev Ankamangidwa

Zimene Zinachitika Pamene M’bale Kuzin ndi M’bale Makhnev Ankamangidwa

Alongo athu 4 akufotokoza mmene zinakhalira pamene apolisi ovala zobisa nkhope anachita chipikisheni m’nyumba zawo mumzinda wa Kaluga ku Russia. Pa nthawiyo, M’bale Kuzin ndi M’bale Makhnev anamangidwa n’kuikidwa m’ndende. Loya wa abalewa akufotokozanso zina.