Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

APRIL 23, 2014
RUSSIA

Anthu Ena ku Russia Akuphwanyiridwa Ufulu Wawo Wolambira

Anthu Ena ku Russia Akuphwanyiridwa Ufulu Wawo Wolambira

Akuluakulu a boma la Russia m’dera la Taganrog, akuphwanya ufulu wolambira wa anthu a Mboni za Yehova powaimba milandu. Kodi n’chiyani chikuchititsa zimenezi? Kodi boma likufuna kuyambiranso kuzunza a Mboni?