Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Russia

 

2020-06-25

RUSSIA

Palibe Chifukwa Choti Tiziopa Kuzunzidwa

Pamsonkhano wapachaka wa 2019 , M’bale Mark Sanderson wa m’Bungwe Lolamulira anakamba nkhani yamutu wakuti, “Kodi Tiziopa Ndani?” Munkhaniyi munalinso vidiyo imeneyi yosonyeza abale ndi alongo athu ku Russia akufotokoza zimene zinawathandiza kuti asamaope kuzunzidwa.

2020-06-02

RUSSIA

Abale Athu Anasonyeza Chikhulupiriro Cholimba Atamenyedwa M’ndende ya ku Orenburg

M’vidiyoyi muli abale ochokera mumzinda wa Saratov ku Russia omwe anamangidwa komanso kuikidwa m’ndende chifukwa za zimene amakhulupirira. Alonda a ndende anamenya abalewa ndi zibonga. Chifukwa choti abalewa amadalira kwambiri Yehova, anapemphera ndipo anakwanitsa kupirira, kupeza mtendere ndi chimwemwe.