Venezuela
Mmene Zinthu Zilili Panopa ku Venezuela: Ntchito ya a Mboni za Yehova Ikupitabe Patsogolo Ngakhale Kuti Mavuto Sakutha
Ngakhale kuti zinthu zafika poipa, a Mboni za Yehova ku Venezuela akupitiriza kugwira ntchito yolalikira molimba mtima.
Mmene Zinthu Zilili Panopa ku Venezuela: A Mboni Ndi Okhulupirikabe Ngakhale Akukumana ndi Mavuto a Zachuma
Ngakhale kuti mavuto azachuma akupitirizabe ku Venezuela, a Mboni za Yehova m’dzikoli akupitirizabe kutumikira Yehova mokhulupirika.