Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Makhalidwe Oipa

Makhalidwe oipa savuta kuwayamba koma zimavuta kuwasiya. Gawo lino lifotokoza ena mwa makhalidwe oipa komanso zimene mungachite kuti muwasiye n’kuyamba kuzolowera kuchita zinthu zabwino.

Kulankhulana

Kodi Ndingatani Kuti Ndithetse Miseche?

Ngati anzanu ayamba kulankhula zonyoza kapena zoipa za anthu ena, musayankhire nawo koma sinthani nkhaniyo!

Kodi Kutukwana N’koipadi?

Popeza kuti anthu ambiri amatukwana, kodi tinganene kuti n’koipadi?

Zizolowezi

N’chifukwa Chiyani Ndiyenera Kupewa Kuonerera Zolaula?

Kodi kuonera zolaula n’kofanana motani ndi kusuta fodya?

Zimene Zingakuthandizeni Kuti Muzipewa Kuonera Zolaula

N’chifukwa chiyani pulogalamu yoteteza kuonera zolaula pa Intaneti siyokwanira?

Kodi Mukulephera Kusiya Kuonerera Zinthu Zolaula?

Baibulo lingakuthandizeni kuti mumvetse cholinga cha zinthu zolaula.

Musawononge Moyo Wanu Chifukwa cha Kusuta

Anthu ambiri amasuta kapena kuvepa. Komabe ena asiya ndipo enanso akufunitsitsa kusiya. N’chifukwa chiyani akuchita zimenezi? Kodi kusuta kungawonongedi moyo wanu?

Kodi Ndingatani Kuti Ndisamagonje Poyesedwa?

Onani zinthu zitatu zimene zingakuthandizeni kuti musamagonje mukayesedwa.

Mungatani Kuti Musamagonje Mukakumana ndi Mayesero?

Mwamuna komanso mkazi weniweni amatha kupewa mayesero. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zinthu 6 zimene zingakuthandizeni kusagonja mukamayesedwa komanso kuti musakhale ndi nkhawa chifukwa chodziwa kuti mwagonja.

Kugwiritsa Ntchito Bwino Nthawi

Kodi Ndi Bwino Kumachita Zinthu Zingapo Nthawi Imodzi?

Kodi mungathedi kumachita zinthu zina nthawi imodzi popanda kusokonezeka?

Kodi Ndingatani Kuti Ndisamachite Zinthu Mozengereza?

Werengani malangizo amene angakuthandizeni kuti musamachite zinthu mozengereza