Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

KODI BAIBULO LIMAPHUNZITSA CHIYANI? (ZOKUTHANDIZANI POPHUNZIRA)

N’chifukwa Chiyani Mulungu Amalola Kuti Anthu Azivutika? (Gawo 2)

Pepalali likuthandizani kumvetsa chifukwa chimene Mulungu amalolera kuti anthu azivutika ndiponso mmene zimenezi zimasonyezera kuti Mulungu ndi wanzeru.