Pitani ku nkhani yake

KODI BAIBULO LIMAPHUNZITSA CHIYANI KWENIKWENI? (ZOKUTHANDIZANI POPHUNZIRA)

Zimene Mungachite Kuti Mulungu Apitirize Kukukondani (Gawo 1)

Zokuthandizani pophunzirazi zachokera m’mutu 19 wa buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?

Kodi tingasonyeze bwanji kuti timakonda Mulungu? N’chiyani chimapangitsa Mkhristu kuti azikonda Mulungu?