Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Zoti Muchite Pophunzira Baibulo

Mulungu Amadana ndi Zinthu Zopanda Chilungamo

Mungaphunzire zambiri pa nkhani yokhudza Ahabu, Yezebeli, Naboti ndi Eliya. Koperani nkhani ya m’Baibuloyi, iwerengeni, ndipo muiganizire mozama n’kuona mmene ingakuthandizireni.