ZOTI MUCHITE Zofunika Kuganizira pa Nkhani ya Chibwenzi YAMBANI Pepalali lingakuthandizeni kuti musayambe chibwenzi ndi munthu yemwe samakukondani. Pangani Dawunilodi Nkhani Zina Zoti Achinyamata Achite Achinyamata Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA Kodi Ndi Mnzanga Chabe Kapena Amandifuna?—Gawo 1: Kodi Ndikuona Zizindikiro Zotani? Nkhaniyi ingakuthandizeni kuti mudziwe ngati munthu amakukondani kapena akungofuna kukhala mnzanu chabe. ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA Kodi Ndi Mnzanga Chabe Kapena Amandifuna?—Gawo 2: Kodi Ndikumukopa? Kodi mnzanuyu angaganize kuti mukumufuna chibwenzi? Zimene zingakuthandizeni. MAVIDIYO AMAKATUNI Kodi Ndi Chikondi Chenicheni Kapena Kungotengeka Maganizo? Onerani vidiyoyi kuti mudziwe tanthauzo la kutengeka maganizo ndiponso chikondi chenicheni. ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA Kodi Kukopana Kuli Ndi Vuto? Kodi kukopana n’kutani? N’chifukwa chiyani anthu ena amakopana? Kodi kukopana kuli ndi vuto? ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA Kodi Ndine Wokonzeka Kukhala Pachibwenzi? Mfundo 5 zimene zingakuthandizeni kudziwa ngati muli wokonzeka kukhala pachibwenzi komanso kulowa m’banja Patsani ena Patsani ena Zofunika Kuganizira pa Nkhani ya Chibwenzi ZOTI ACHINYAMATA ACHITE Zofunika Kuganizira pa Nkhani ya Chibwenzi Chichewa Zofunika Kuganizira pa Nkhani ya Chibwenzi https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/502016173/univ/art/502016173_univ_sqr_xl.jpg