Posita: Ndi Ndani Angakhale Mnzanga?
Positayi ingakukumbutseni kufunika kosankha anzanu omwe amakonda Yehova.
Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi
KHALANI BWENZI LA YEHOVA
Phunziro 47: Ndi Ndani Angakhale Mnzanga?
Yehova amafuna kuti ukhale ndi anzako, koma kodi ungasankhe bwanji anzako abwino?
ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA
Zoti Ana Achite
Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.