Buku la Mulungu Ndi Chuma
Baibulo ndi mphatso yochokera kwa Yehova. Tiyeni tione zomwe tingaphunzire tikamaliwerenga.
Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi
KHALANI BWENZI LA YEHOVA
Buku la Mulungu—Ndi Chuma (Nyimbo 96)
Timaphunzira zambiri zokhudza Yehova komanso tsogolo lathu tikamawerenga mawu a Mulungu
ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA
Zoti Ana Achite
Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.