Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Lowezani Salimo 133:1

Lowezani Salimo 133:1

Mukaimba nyimbo nambala 20, kongoletsani tsambali ndi chekeni. Kenako lowezani lemba la Salimo 133:1, kuti likuthandizeni kukumbukira zoti misonkhano yathu ndi yofunika kwambiri.

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

KHALANI BWENZI LA YEHOVA

Dalitsani Msonkhano Wathu (Nyimbo Nambala 20)

Muimbe nawo nyimboyi ndipo onani zimene anzanu ena amachita kuti azisonkhana ndi Akhristu anzawo nthawi zonse.

ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA

Zoti Ana Achite

Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.