Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Yerekezerani Kuti Muli M’dziko Latsopano

Yerekezerani Kuti Muli M’dziko Latsopano

M’dziko latsopano tidzasangalala ndi zinthu zambiri. Tiyeni tikambirane zinthu ziwiri.

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

KHALANI BWENZI LA YEHOVA

Yerekezerani Kuti Muli M’dziko Latsopano (Nyimbo 139)

Nyimbo yabwino kwambiri imene ingakuthandizeni kudziona muli m’paradaiso m’tsogolo ndipo Mulungu atasintha zinthu zonse kukhala zatsopano.

ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA

Zoti Ana Achite

Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.