ZOCHITA PA KULAMBIRA KWA PABANJA
Gwiritsani ntchito nkhani ya zithunzi zofotokoza nkhani ya m’Baibulo ya Rahabi ndi kugwa kwa mzinda wa Yeriko komanso zochita zitatuzi kuti muphunzitse ana anthu mwanjira yakuti azikhala ngati akuona zimene zikuchitikazo.