ZOTI MUCHITE POPHUNZIRA Msasa wa Aisiraeli YAMBANI Koperani nkhaniyi kuti mukonze msasa wa Aisiraeli pa nthawi imene anali m’chipululu. Koperani Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi ZOTI ANA ACHITE POPHUNZIRA Aisiraeli Analowa M’dziko la Kanani Chitani masewera ofananitsa makadi pogwiritsa ntchito nkhani ya pa Yoswa chaputala 2 mpaka 7 kuti muone ngati mukukumbukira. ZOTI ANA ACHITE POPHUNZIRA Imbani Nyimbo Yothandiza Kukhala Olimba Mtima Phunzirani nyimbo imene imatithandiza kukhala olimba mtima ndipo kenako muimbe limodzi ndi banja lanu. ZOTI ANA ACHITE POPHUNZIRA Kodi Mungalimbikitse Ndani? Zochitazi zingathandize ana a pakati pa zaka 8 ndi 12 kuti adziwe zimene angachite kuti alimbikitse munthu. Patsani ena Patsani ena Msasa wa Aisiraeli ZOTI ANA ACHITE POPHUNZIRA Msasa wa Aisiraeli Chichewa Msasa wa Aisiraeli https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/502014301/univ/art/502014301_univ_sqr_xl.jpg