Zoti Muchite Pophunzira Mayina a Ana a Yakobo YAMBANI Koperani nkhaniyi ndipo pezani mayina a ana atatu a Yakobo amene akufotokozedwa. Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi ZOTI ANA ACHITE POPHUNZIRA Aisiraeli Analowa M’dziko la Kanani Chitani masewera ofananitsa makadi pogwiritsa ntchito nkhani ya pa Yoswa chaputala 2 mpaka 7 kuti muone ngati mukukumbukira. ZOTI ANA ACHITE POPHUNZIRA Imbani Nyimbo Yothandiza Kukhala Olimba Mtima Phunzirani nyimbo imene imatithandiza kukhala olimba mtima ndipo kenako muimbe limodzi ndi banja lanu. ZOTI ANA ACHITE POPHUNZIRA Kodi Mungalimbikitse Ndani? Zochitazi zingathandize ana a pakati pa zaka 8 ndi 12 kuti adziwe zimene angachite kuti alimbikitse munthu. Patsani ena Patsani ena Mayina a Ana a Yakobo ZOTI ANA ACHITE POPHUNZIRA Mayina a Ana a Yakobo Chichewa Mayina a Ana a Yakobo https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/502013157/univ/art/502013157_univ_sqr_xl.jpg