Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?

Mbalame Zoimba Nyimbo

Mbalame Zoimba Nyimbo

Pa nyama zonse, mbalame zokha ndi zimene zili ndi timinofu tam’mbali mwa paipi ya mpweya, tomwe zimagwiritsa ntchito poimba nyimbo zomveka bwino komanso zosiyanasiyana.