Zokuthandizani za pa Intaneti
Mmene Mungagwiritsire Ntchito JW.ORG
Phunzirani mmene mungagwiritsire ntchito mbali zosiyanasiyana za pawebusaiti ya jw.org. Gwiritsani ntchito ndondomeko komanso mfundo zokuthandizani kutsegula, kufufuza ndiponso kupanga dawunilodi zinthu. Pezani mayankho a mafunso okhudza jw.org.
JW Library
Werengani ndi kuphunzira Baibulo pogwiritsa ntchito Baibulo la Dziko Latsopano. Yerekezerani zimene Mabaibulo ena amanena.
JW Library Sign Language
Gwiritsani ntchito pulogalamu yathu yapazipangizo za m’manja kuti mupange dawunilodi, kusunga komanso kuonera Baibulo komanso mabuku ndi zinthu zina za m’chinenero chamanja.
Watchtower Library
Muli Mabaibulo a zinenero zosiyanasiyana, mabuku, komanso zinthu zofufuzira pophunzira Baibulo.
JW Language
Pulogalamu yothandiza pophunzira chineneroyi, ili ndi magawo othandiza polalikira anthu m’zinenero zosiyanasiyana. Magawowa ndi monga mawu ojambulidwa a chinenero chimene mukuphunzira komanso kudziwa tanthauzo la mawu a chinenero china.