JW Language
Pulogalamu yophunzirira chinenero ya pa JW inakonzedwa ndi a Mboni za Yehova kuti izithandiza anthu amene akuphunzira chinenero kuti azidziwa mawu ambiri a chinenerocho komanso mmene angachilankhulire muutumiki komanso m’misonkhano.
Zinthu Zopezeka pa JW Language
Phunzirani mmene mungagwiritsire ntchito zinthu zopezeka mupulogalamuyi.
Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri Okhudza JW Language (Pa Zipangizo za Android)
Pezani mayankho a mafunso omwe anthu amafunsa kawirikawiri.
Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri Okhudza JW Language (Pa Zipangizo za iOS)
Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri
Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri Okhudza JW Language (Pa Zipangizo za Windows)
Pezani mayankho a mafunso omwe anthu amafunsa kawirikawiri.