Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Maulaliki Acitsanzo

Maulaliki Acitsanzo

GALAMUKANI!

Kugaŵila Cofalitsa: Ndakubweletselani Galamukani! iyi yatsopano.

Funso: Onani funso ili patsamba 2. Kodi muganiza bwanji?

Lemba: Luka 7:35

Nkhani iyi ifotokoza mmene mfundo imeneyi ilili yoona ponena za Baibulo.

GALAMUKANI!

Funso: Kodi muvomeleza kuti mau awa ndi ofunika kuwatsatila?

Lemba: Mat. 6:34

Kugaŵila Cofalitsa: [Pezani nkhani yakuti “Lingaliro la Baibulo—Nkhawa.”] Nkhani ino ionetsa mmene Baibulo lingatithandizile kulimbana ndi nkhawa.

Zimene Baibo Imaphunzitsa

Funso: Anthu amene amakhulupilila Mulungu amafuna kumuyandikila. Kodi mudziŵa kuti Baibulo limatilimbikitsa kuyandikila Mulungu?

Lemba: Yak. 4:8a

Kugaŵila Cofalitsa: Buku ili linapangidwa kuti litithandize kudziŵa zambili za Mulungu mwa kuseŵenzetsa Baibulo. [Fotokozani mfundo za m’nkhani 1 m’buku la Zimene Baibo Imaphunzitsa.]

LEMBANI ULALIKI WANU

 

Onani maulaliki acitsanzo amene asonyezedwa kale kuti akuthandizeni kulemba ulaliki wanu.