Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

April 11-17

YOBU 21-27

April 11-17
  • Nyimbo 83 ndi Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Yobu Anapewa Maganizo Olakwika”: (Mph. 10)

    • Yobu 22:2-7—Elifazi anapeleka uphungu popanda umboni weniweni ndipo anacita za m’mutu mwake (w06-CN 3/15 15 ndime 7; w05-CN 9/15 26-27; w95-CN 2/15 27 ndime 6)

    • Yobu 25:4, 5—Bilidadi anakamba maganizo olakwika (w05-CN 9/15 26-27)

    • Yobu 27:5, 6—Yobu sanalole kuti anthu ena amupangitse kuganiza kuti walephela kusunga umphumphu (w09-CN 8/15 4 ndime 8; w06-CN 3/15 15 ndime 9)

  • Kufufuza Cuma Cakuuzimu: (Mph. 8)

    • Yobu 24:2—N’cifukwa ciani kusuntha malile kunali mlandu waukulu? (it-1 E 360)

    • Yobu 26:7—Kodi Yobu analifotokoza bwanji dziko lapansi? (w15-E 6/1 5 ndime 4; w11-CN 7/1 26 ndime 2-5)

    • Kodi kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwandiphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ndi mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingagwilitsile nchito mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: Yobu 27:1-23 (Mph. 4 kapena zocepelapo)

KUONJEZELA LUSO LANU MU ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: Galamukani! ya 2016 Na. 2 cikuto. Yalani maziko a ulendo wobwelelako. (Mph. 2 kapena zocepelapo)

  • Ulendo Wobwelelako: Galamukani! ya 2016 Na. 2 cikuto. Ndiyeno yalani maziko a ulendo wina wobwelelako. (Mph. 4 kapena zocepelapo)

  • Phunzilo la Baibulo: bh 145 ndime 3-4 (Mph. 6 kapena zocepelapo)

UMOYO WATHU WACIKRISTU

  • Nyimbo 129

  • Kugonjetsa Munthu Amene Akukuvutitsani Popanda Kumenyana Naye: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani kavidiyo ka tukadoli kakuti, Kugonjetsa Munthu Amene Akukuvutitsani Popanda Kumenyana Naye. (Pitani pa jw.org ndi kuona polemba kuti BIBLE TEACHINGS > TEENAGERS.) Mukatsiliza, kambilanani mafunso otsatilawa: N’ciani cimacititsa munthu kuvutitsidwa? Kodi munthu amene amavutitsidwa amakhala ndi maganizo olakwika ati? Kodi mungapewe bwanji anthu amene amakuvutitsani? Kodi muyenela kuuza ndani ngati munthu wina akukuvutitsani? Chulani mfundo zina za m’buku la Acicepele Akufunsa Voliyumu 2 mutu 14.

  • Phunzilo la Baibulo la Mpingo: ia mutu 13 ndime 1-12 (Mph. 30)

  • Kubweleza Mfundo Zimene Taphunzila ndi Kufotokoza Zimene Tidzaphunzila Mlungu Wotsatila (Mph. 3)

  • Nyimbo 23 ndi Pemphelo