Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

April 18-24

YOBU 28-32

April 18-24
  • Nyimbo 17 ndi Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Yobu Anali Citsanzo Cabwino Pankhani Yosunga Umphumphu”: (Mph. 10)

    • Yobu 31:1—Yobu anacita “pangano” ndi maso ake (w15-CIN 6/15 16 ndime 13; w15-CIN 1/15 25 ndime 10)

    • Yobu 31:13-15—Yobu anali wodzicepetsa, wolungama, ndi wacifundo (w10-CN 11/15 30 ndime 8-9)

    • Yobu 31:16-25—Yobu anali kuthandiza anthu osoŵa (w10-CN 11/15 30 ndime 10-11)

  • Kufufuza Cuma Cakuuzimu: (Mph. 8)

    • Yobu 32:2—Kodi Yobu anaonetsa kuti “anali wolungama, osati Mulungu” m’njila iti? (w15-CN 7/1 12 ndime 2; it-E 1 606 ndime 5)

    • Yobu 32:8, 9—N’cifukwa ciani Elihu anaona kuti afunika kukambapo ngakhale kuti anali wamg’ono pa gulu la anzake? (w06-CN 3/15 16 ndime 1; it-2 E 549 ndime 6)

    • Kodi kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwandiphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ndi mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingagwilitsile nchito mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: Yobu 30:24–31:14 (Mph. 4 kapena zocepelapo)

KUONJEZELA LUSO LANU MU ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: Galamukani! ya 2016 Na. 2 tsa. 12-13. Ndiyeno yalani maziko a ulendo wobwelelako. (Mph. 2 kapena zocepelapo)

  • Ulendo Wobwelelako: Galamukani! ya 2016 Na. 2 tsa. 12-13. Yalani maziko a ulendo wina wobwelelako. (Mph. 4 kapena zocepelapo)

  • Phunzilo la Baibulo: bh 148 ndime 8-9 (Mph. 6 kapena zocepelapo)

UMOYO WATHU WACIKRISTU

  • Nyimbo 115

  • Phunzilani pa Kukhulupilika kwa Ena (1 Pet. 5:9): (Mph. 15 kapena zocepelapo) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Harold King: Remaining Faithful in Prison. (Pitani pa tv.pr418.com, ndi kuona polemba kuti VIDEO ON DEMAND > INTERVIEWS AND EXPERIENCES.) Pambuyo pake, kambilanani mafunso otsatilawa: Kodi M’bale King anapitiliza bwanji kukhalabe munthu wauzimu pamene anali m’ndende? Kodi kuimba nyimbo za Ufumu kungatithandize bwanji kupilila mavuto? Kodi citsanzo cabwino ca kukhulupilika ca M’bale King cakulimbikitsani bwanji? Ngati n’zosatheka kuonelela vidiyo, seŵenzetsani mfundo zopezeka mu Nsanja ya Mlonda ya February 15, 2015 tsamba 32 ndime 3, ndi Nsanja ya Olonda ya September 15, 2003 tsamba 15 ndime 3, kuti muyankhe mafunso.

  • Phunzilo la Baibulo la Mpingo: ia mutu 13 ndime 13-25, ndi kubwelelamo pa tsa. 114 (Mph. 30)

  • Kubweleza Mfundo Zimene Taphunzila ndi Kufotokoza Zimene Tidzaphunzila Mlungu Wotsatila (Mph. 3)

  • Nyimbo 81 ndi Pemphelo