Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YOBU 28-32

Yobu Anali Citsanzo Cabwino Pankhani Yosunga Umphumphu

Yobu Anali Citsanzo Cabwino Pankhani Yosunga Umphumphu

Yobu anali wokonzeka kutsatila mfundo za Yehova za makhalidwe abwino

31:1

  • Yobu sanayang’ane mkazi wina momusilila, kupatulapo mkazi wake

Yobu anali citsanzo cabwino pocita zinthu ndi ena

31:13-15

  • Anali wodzicepetsa, wolungama, ndi wacifundo. Anali kuganizila anthu onse, kaya ndi olemela kapena osauka

Yobu anali wopatsa, osati wodzikonda

31:16-19

  • Anali kuthandiza anthu ovutika